3087
·
info@ucssacco.com
·
Mon - Fri 08:00 - 15:30 | Sat 08:00 - 11:00
Login Account

OUR VIDEOS

OUR VIDEOS

11

Tsegulani account ya bizinezi yotchedwa Tipindule SME ku United Civil Servant SACCO kuti mukhale ndi mwayi osunga ndalama za bizinezi yanu komanso mwayi wotenga ngongole.

11

The new funeral cover consists four premiums with different benefits. Members can choose any premium of there choice. 

11

In 2024 United Civil Servants SACCO conducted a number of activities aimed at changing people’s lives.

11

With Ulimi loan, you can get agricultural inputs such as seeds, and fertilizer without any upfront costs. Get Ulimi loan and focus on farming with ease of mind.

11

Come to United Civil Servants SACCO and top up your loan with Mzati-Topup

11

Lowani United Civil Servants SACCO kuti mukhale ndi mwayi otsegula Tipindule SME account yomwe imathandiza kutukula business yanu.

11

Ngati muli membala wa United Civil Servants SACCO ndipo mumachita bizinezi, tsegulani account ya padera yosungako ndalama za bizinezi ndipo mudzakhala ndi mwayi wotenga ngongole mpaka K20 million kwacha malingana ndi ndalama zomwe mukusunag Ku account ya bizinezi yanu komanso phindu komwe mukupanga pa bizinezi yanu.

11

Mukasunga ndalama ku United Civil Servants SACCO zidzakhala zotetezeka ndipo kumapeto kwa chaka mudzalandira ma dividend.

11

Kuno ku United Civil Servants SACCO kuli ngongole zosiyanasiyana zomwe mungathe kutenga malingana ndi kuthekera kwanu. Khalani membala wa United Civil Servants SACCo lero kuti muthe kutenga ngongolezi.

11

An array of our affordable loans. Get in touch and let us help you achieve your financial goals

11

Phindu ili ku United Civil Servants SACCO! Pangani Chisankho chosunga ndalama ndi ifeyo ndipo muzalandira ma dividend ochuluka zedi. Kuonjezerapo, United Civil Servants SACCO imagwira pa nkono ma membala ake muyengo yazovuta

11

Members explaining how UCS SACCO has helped them achieve their goals.